Ndithokoza Amai (Mama Siyabonga)

Taonani Nkhuku
Ikamaikila Madzila ake
Imawafungatira
Kufikila kuswa Ana ake
Imawatetezanso
Kutizilombo ndi nyama Zosiyana
Eeeeh yeah

(Mama Siyabonga, Mama Siyabonga)
(Mama Siyabonga, Pondibeleka)
(Mama Siyabonga, Mama Siyabonga)
(Mama Siyabonga, Pondibeleka)

Chimodzi modzinso
Mai kwa Mwana wake
Amamusamala
Kufikila Kukula Kwake
Amamutetezanso
Kumatenda ndi Zinthu
Zina Zosiyana
Eeeeh yeah

(AMai Ndikuthokoza, Amai Ndithokoza inu)
(Amai ndikuthokoza inu Pondibeleka)
(AMai Ndikuthokoza, Amai Ndithokoza inu)
(Amai ndikuthokoza inu Pondibeleka)

(Mama Siyabonga, Mama Siyabonga)
(Mama Siyabonga, Pondibeleka)
(Mama Siyabonga, Mama Siyabonga)
(Mama Siyabonga, Pondibeleka)

Taonani Nkhuku
Ikamaikila Madzila ake
Imawafungatira
Kufikila kuswa Ana ake
Imawatetezanso
Kutizilombo ndi nyama Zosiyana
Eeeeh yeah

(AMai Ndikuthokoza, Amai Ndithokoza inu)
(Amai ndikuthokoza inu Pondibeleka)
(AMai Ndikuthokoza, Amai Ndithokoza inu)
(Amai ndikuthokoza inu Pondibeleka)



Credits
Writer(s): Edward Manuel Correia
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link