Dear kim (Why challenge)

Dear Kim
Lero mahope ndalimba mtima
Ndikuwuza olo ngakhale wafilla wina
Koma mwina
Ukamva verse yi usintha
Undipasa ka nthawi kokha tsiku lina
First day kukuona ine sinnali bho
Utandiyankha moni ndinazimva u goat
Olo blage namuwuza ankayesa ndi jokes
Ndinali ku timveni ndakumana mmahope
Paja umakonda ngende Eti?
Lemme tell you girl your talent I do appreciate
Timawu Tako tanthetemya
Ndithudi namalenga
AnaTumiza ngelo kuti ine ndizipenga

Tell me why
Tell me why
Sitingangocheza
Tell me why

Tell me why
Tell me why
Sumufila short guy
Tell me why

Tell me why
Tell me why



Credits
Writer(s): Joy Gondwe
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link