Kamiliyoni (feat. Doumen9)

Yaah!
Kulikonse ungapite ine ndikulondola
Chilichonse ungafune ine ndikupangila
Kwanu ndikafikabe
Shawty i wanna be your commando
Kwanu ndikafukabe
Mama i wanna be your commando
Ndiwe fine girl
Ndiwe cool girl
Umabweletsa chimwemwe, mtendele
Ndiwe fine girl
Ndiwe cool girl
Umabweletsa chimwemwe, ndi mtendele!

My love for you ndi one in a million yeh
Zoku player no no
No more za kamiliyoni yeh
Zachibwana ndakana
Ukhale wanga mpaka wana
Iwe mama ine papa
Iwe ndi ine timanvana wooh
My love for you ndi one in a million yeh (one in a million yeh!)
Zoku player no no
No more za kamiliyoni yeh (no more za kamiliyoni!)
Zachibwana ndakana
Ukhale wanga mpaka wana
Iwe mama ine papa
Iwe ndi ine timanvana wooh



Credits
Writer(s): Andrew Ngwala, Paul Xander
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link