Udani

Kudabwa
Nthawi zina ndima dabwa
Wanga anthu momwe ama khala
Kubaba mtima wanga uma baba
Ubaba anthu zomwe ama panga
Kudana anthu awa ama dana
Sibanja ine mango khala

Mwina ndi nyanga zomwe wina ana panga
Kapena sinyanga nakuba kapena chabe nikaduka
Kamene kalengesa banthu bamozi kupeza vifukwa
Cifukwa mayeso fufuza koma sina peze cifukwa eh
Kunjako nko kudha macita mantha ndi khalidwe yawa
Udani waconco wacoka kuti ma lankhulana
Pempelo yanga niyoti izozo ma lalilane
Nanga cikondi munali naco cinapita kuti
Funso

Kudabwa
Nthawi zina ndima dabwa
Wanga anthu momwe ama khala
Kubaba mtima wanga uma baba
Ubaba anthu zomwe ama panga
Kudana anthu awa ama dana
Sibanja ine mango khala

Kumakhalila midesu
Ena akulila Yesu
Mundisamalile ana banja isa pwasuke tikhale ifeso
Ogwilizana despite what we facing I hope we don't break us ineo
Pemphelo yanga ndiyoti udani ulipo kuntima uthepo
Koma zukhala nga e sizotheka anthuwa afuna afepo
Udani waconco ku opya Ambuye kumwamba muyanganilepo
Kuma kangana pa zopanda phindu poka poka ena afepo
Anthu wa ndani aloza umbuli wa conci ine sina onepo

Kudabwa
Nthawi zina ndima dabwa
Wanga anthu momwe ama khala
Kubaba mtima wanga uma baba
Ubaba anthu zomwe ama panga
Kudana anthu awa ama dana
Sibanja ine mango khala



Credits
Writer(s): Chimwemwe Zulu
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link