Link Up

Link up
Link up
Link up

Can we link up
Ubwere ndi zi kush ndizi liquor
Ubwere ndi anzako timenye drink up
Titha kufika mawa ngati mukulimba
Ti blowe cash ti blowe kush ti blowe shisha

Patricia ndi jesse koma osati lingard
Way she wine ngati glass ya linga
Koma sungamkwere ngati mtengo wa minga
Ndi oopya heavy deni ya msing'anga
Nfana oyela heavy ngati zi mkaka
Takin shots after shots mpaka ndi blacka
Gist ili ball apa ndimaka
She make man a go mushy
Amashala chaku ku north ngati zephyr
Zodiac sign ndika leo ngati lev
Zambian girls ati ndili mushe

Link up
Ubwere ndi zi kush ndizi liquor
Ubwere ndi anzako timenye drink up
Titha kufika mawa ngati mukulimba
Ti blowe cash ti blowe kush ti blowe shisha
Can we link up
Ubwere ndi zi kush ndizi liquor
Ubwere ndi anzako tizamenye drink up
Titha kufika mawa ngati mukulimba

Am the coolest kid in malawi
Kamuzu banda wangozaza mu baggie
Rose chiwambo ango twerka ngati cardi
Chilembwe ndi bingu ango fila ku side b
Ubwere ndi nzako tizamenye 3 some
Kuziwakale deal nde dinculm
Life is too short when you having fun
Moti apapa ikutsika mmene ukundi kissa mu
Mad love from chitipa to nsanje
Straight from africa thats malawi
Egyptian ting how am rolling with mummies
Sweet like candy wine fi daddy
She a baddie og she dont copy nobody
265 mdubs to the world

Link up
Ubwere ndi zi kush ndizi liquor
Ubwere ndi anzako timenye drink up
Titha kufika mawa ngati mukulimba
Ti blowe cash ti blowe kush ti blowe shisha
Can we link up
Ubwere ndi zi kush ndizi liquor
Ubwere ndi anzako timenye chi drink up
Titha kufika mawa ngati mukulimba



Credits
Writer(s): Chifundo Chingaipe
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link