Amuna ndi Agalu (feat. Same Cris)

Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dododo
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are do do do

Ndimafuna mamuna wabho
Wa ma lux owoneka bho
Osanyasa ngati akudya mandimu
Six pack adzivaya gym
Adzitchena ngati akakwela ndege
Woti azimzanga asamandiseke
Azindipanga support ngati jeke
Oteleyo nde sindingamuleke
Mamuna adzikhalangati wa zee world
Ozitsata chikondi adzichidziwa
Adzikunyengelela ukakwiya
Bea please am sorry ndasiya
Akhale ovaya heavy akhale ndi Money ne ne
Akhale ndi galimoto iliyonse kaya ndi Benenene
Please call pompo adziyimba phone
Sindikufuna mamuna wangati John
Anangondivulavula mkunditaya
Kundibulabula mkundiponya kumtaya
Anangonditupitsa mkubanduka
Anangondiphulitsa ndi Bazuka
Amuna ndi agalu samaseka amaluma ukapusa amakupanga Geoffrey

Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dododo
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are do do do

Ndimabwera ndi chi bodza kuti
Pa ukwati dzakuveka velo komaso ndidzatchena suit
Pasi pake dzavala sapato yokwiya ankle Buti
Kenako waku photo shoot
Kundipanga trust ndikulola
Posapanga invest ndikolola
Sakudziwa mene wandiputa ine
Ndine Ronaldinho ndimadodadada
Amabwera pa deni atatchena mmaso mwake ataphodadada
Amayesetsa kuchengetela
Koma sindisiya kutchetchelela
Mkazi wachimbina kupemelela
Nde choncho sindisekelela
Ndendende ma girls eti
Mudziwonetsetsa ofuna kupanga date
Amuna ndi agalu amafuna kutsitsa weight
Kenako kukutaya toilet
Ana ena amakhala opanda bambo
Chifukwa chosakhala ndi chisakho
Osatengeka ndi Jumbo Rambo
Kapena usipa micheni ndi chambo

Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dododo
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu huuu huuu
Men are do do do
Amuna ndi agalu huuuuu
Men are dogs
Amuna ndi agalu uhuuuuu
Men are do do do



Credits
Writer(s): Henry Kanjanga
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link