Chikondi (feat. Niekay)

Wina atikonda ife
Bwenzi lathu ndi Iyeyu
Atifunafuna ife inde nthawi zonsetu
Atifunafuna ifetu
Ndani mwa abale athu akanatifera ife
Koma Yesu m'malo mwathu
Anapachikidwatu
Anapachikidwa oh

Chikondano chakechi nchachikulukuludi
Chikondicho cha Yesu nchachikulukuludi

Timchimwira kopambana
Ndi kumusawutsa Iye
Koma Bwenzi lathu Yesu
Atikondakonda ife
Atikonda
Mtiphunzitse Mbuye Yesu
Tikondane nanudiu
Tisayiwalire konse
Bwenzi lathu ndinutu
Bwenzi lathu

Chikondano chakechi nchachikulukuludi
Chikondicho cha Yesu nchachikulukuludi

Chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu
Chikondi cha Yesu



Credits
Writer(s): Andrew Mijoya
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link