Intro

(Emo D)
Yo

Ndimayenda ndi king Classic
2019 kumenya tour
Kuvaya 'u Mzuzu ku killer show
Kubwerako, kuvaya Ls ku killer so
Kusiya show itadhuwa
Wavy-wavy with the flow
Ma guy akuthoka kuti Gattah uli bho

Satana sakuyimva, akundimenyela call
Adziwa kuti fan base yanga yonse ili bho (ili bho)
Ndikafika pa stage imapenga
Kukhala ngati zamba imatenga
Nanenso nkamabwera ndimatenga
Sinabwere kudzayimba ndudzalengeza uthenga

Show yachibwana sindikupanga
Osamandipanga feature phwanga
Sinanga phwanga sangakhare size yanga
Sindifuna kupweteka aphwanga

Undiphulise dollar
Usandiphulise ngozi phwanga
Brother wanga anaphulisa, ndine Nkozi, phwanga
Gattah, Gattah utipha, of course phwanga
Ndikapanda kupanga ine, nanga ndani azipa-?

Hmm, I think feature ndingokweza ntengo
Chifukwa ma rapper akubwelera ntembo
I think ndikuwapangira business
Abwenzi losaona nyengo
Silidutsa tsiku nsanawone mwendo
Zimachitika game muno nzachilendo
Mwina simunapange notice

Ma rap group anatha inatsala ndi DARE DEVILS
Why?
The difference is the same homie
So never put the blame on me like Mr lonely
And to all the young guys coming up
Make sure opinions from us shouldn't ever be the case homie

I got a queen I will die for
Ngakhale ndikusaka survival
Ndikupanga ngini yomanga ngati Five O
It's my time bro
I need a moment of
Silence



Credits
Writer(s): Stephane David
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link