Anamva

It's the sign of the big league
Sean Morgan on it

Anamva anawa
Zomwe timakamba zija anamva
Zoti mukufuna kuonjeza number
Anamva, anamva Michael number
Zoti mukufuna kundisiya zija amva
Musandifuse ndawapeza akukamba
Akuti zachamba, nde magaye mwamva
Akufuna kutenga mitala kodi mwamva?

Mmh, sitilora no, sitilora no
One man down tizakula bwanji no
Tilipo ana four tizakula bwanji no
Moyo wuzavuta tizakula bwanji no
Eeh, sitilora no, sitilora no
Ndi masten okha tizakula bwanji no
Tilipo ana four tizakula bwanji no
Moyo wuzavuta tizakula bwanji no (yeah)

(Mhu yeah, this life nah)
Ayiwala madala
Ayiwala big man padzana
Ndimavaya pa Kalambo wosadya
Fees imavuta tili pa Kabwabwa
Mlengi anamva kulira pempho lathu anayankha
Ndinavaya MUST, eya komwe ku Ndata
Dolla ikalowa ndimatumiza kwa Mada
Uwapatseko madala akawode mbatata
Wezi wezi, wezi wezi, zinthu zinagwira nsewu
Mpaka big man inagula chapa nsewu
Amasiyanitsa iwo akayenda pansewu
Mkutheka mkaziyu anampeza pansewu
Why now him say he wants another one
Mami amavutikavutika eh kusaka man
Lero zayenda ayiwala komwe achoka man
Akwela njovu ayiwala kuli mame man
Why do people easily forget where dem coming from?
When dem think so if you work amasinthano
Misozi inatsika-tsika-tsika ndinachokapo
Ndinadziwa chikondi cha makolo chiposa zonse (yeah)



Credits
Writer(s): Sean Morgan
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link