Edgar Kapiza Bayani feat. Walusungu Munthali & Coss Chiwalo -
Nyimbo Za Katolik Vol 2. Ndikukondani Mulungu Wanga
Yesu Mbuye Ofatsa (Chichewa Hymn 92)
Ndikupembedza Inu mu Ukaristia (I adore Thee in the Eucharist)
Ndikumverani ndithu Ambuye okoma (Sweet Jesus I listen to you)
Muchita zozizwitsa pakukhala nafe (Miracles abound when you are in our midst)
Chifukwa mutikonda anthu ochimwafe (Because you love us the sinners)
Yesu Mbuye ofatsa mwana wa Mulungu (Meek gentle Jesus son of God)
Idzani Mtima mwanga (Come into my heart)
Mundilere ndinu (And take care of me)

Ambuye okondeka mundifuna ine (Loving Lord you are looking for me)
Muti ndidzakupatsa thupi langa lomwe (with a promise to give me your body)
Koma ine ndachimwa ndili ndi manyazi (But am sinful and ashamed)
Mbuye sindiyenera kukulandirani (I am not worthy to receive you)

Mudalandira kale anthu osauka (You welcome poor people from ancient times)
Nditi mundiyangane ndi kundichiritsa (I ask that you look at and heal me)
Inde Ambuye Yesu mphavu mulinazo (I know you have the healing powers)
Munene mawu anu ndiyere tsopano (Only say a word and I shall be sanctified)

Ambuye mundikonda inu wachisoni (Merciful Lord you truly love me)
Koma sindidziwitsa kukubwenzerani (I don't know how to return the favour)
Ndimati mtima wanga muufuna lero (But perhaps it's my heart you want)
Ndiupereka ndekha kwa Inu tsopano (Freely I give it you)

Credits
Writer(s): Traditonal Hymns
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Link
Other Album Tracks
- Ndikukondani Mulungu Wanga (Chichewa Hymn 79)
- We Charo, Thuuska Chiuta (Tumbuka Hymn 183)
- Idzani Mzimu Olenga (Chichewa Hymn 43)
- Dada Wa Nkhongono Zose (Tumbuka Hymn 228)
- Yesu Mbuye Ofatsa (Chichewa Hymn 92)
- Fumu TIkumuongani (Tumbuka Hymn 268)
- Ife Tonse Tifuna Mulungu (Chichewa Hymn 54)
- Lusungu Fumu (Tumbuka Hymn 40)
- Kumwamba Ndithu Kukoma (Chichewa Hymn 193)
- Transfige Me (LAtin Hymn 24)
All Album Tracks: Nyimbo Za Katolik Vol 2. Ndikukondani Mulungu Wanga >
© 2025 All rights reserved. Rockol.com S.r.l. Website image policy
Rockol
- Rockol only uses images and photos made available for promotional purposes (“for press use”) by record companies, artist managements and p.r. agencies.
- Said images are used to exert a right to report and a finality of the criticism, in a degraded mode compliant to copyright laws, and exclusively inclosed in our own informative content.
- Only non-exclusive images addressed to newspaper use and, in general, copyright-free are accepted.
- Live photos are published when licensed by photographers whose copyright is quoted.
- Rockol is available to pay the right holder a fair fee should a published image’s author be unknown at the time of publishing.
Feedback
Please immediately report the presence of images possibly not compliant with the above cases so as to quickly verify an improper use: where confirmed, we would immediately proceed to their removal.