Experience

Ukaliiiiiii
Heeeeee
Royal hustle the factory
Ndakulandilani chief muma interview muno ine ndi mr czar
Ndikufuna mundiyakhe fuso linalililose sindufuna zobisa
Ngati mukudziwa kuti muli ndimatukutuku muno sitigwilizana
Office ndi yanga introduce yourself mwina mkumvana
Ndine henry ndimagela ku chanco
Ndinakhoza bwino kuposa anzanga
Ngati mukufuna watchito wabho
Ine ndilipo zithu ndipanga
I dont give a damn about what you are saying
Ndayiwona cv sukupangasotu qualify
Of course uli degree koma ulibe experience taziwone sunavale tie

Experience experience experience (My foot)
Experience experience experience (Uko)
Experience experience experience (Yachani)
Experience experience experience (Ndilibe)
Experience (Igwa kumwamba)
Experience (Ndingoyitola)
Experience (Ibwera yokha)
Experience (Ichoka Ku)
Experience (Igwa kumwamba)
Experience (Ndingoyitola)
Experience (Ibwera yokha)
Experience (Ichoka Ku)

Experience ndipeza bwanji
Munthu ine school ndamaliza last year
Ntchito ndayisaka town mu
Kumangozungulilamo ngati ndine wa masiye
Nanga mpaka five years experience
Ichoka kuti ndine mwanapiye
Mwana wang'ono osakhwima pamchombo
Chonde bwana musandisiye
Ndimene zikukhalila mma office mu
Ngati ulibe experience sukupeza tchitozi
Graduates every year mu ma college mu
Koma tchito zikusowa lower case in capitals
Ena kulowela connection, mpaka connection
Eya mumadziwa ndani nkozi
Mkazi avule kaye kuti alowe apo bii kulibe ntchito boss
Ati umakhala kuti (Biwi)
Kumudzi kwanu ndikuti (Ntcheu)
Oooh ndiwe ngoni
Tchito yi siyukapanga suit
Iwe yukupanga gwanda
Kuno timalemba anthu akuzomba
Nde paja wati siwe wakuzomba
Olo ukasake experience vephi sitidzakulemba

Experience experience experience (My foot)
Experience experience experience (Uko)
Experience experience experience (Yachani)
Experience experience experience (Ndilibe)
Experience (Igwa kumwamba)
Experience (Ndingoyitola)
Experience (Ibwera yokha)
Experience (Ichoka Ku)
Experience (Igwa kumwamba)
Experience (Ndingoyitola)
Experience (Ibwera yokha)
Experience (Ichoka Ku)



Credits
Writer(s): Henry Kanjanga
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link