Sangalala (feat. Molto Zambia)

Yeo abanja, Kaya mwayamba?
Yeo tsono abanja ninali kuganizila ngati,
Munthu kukhala osangalala uyenera khala mpondamatiki
Koma ayi zonse zili mbongo

Ine ndinali kufunako chengelo koma ayesu andipatsa chigayo
Ine ndinali kufunako chengo koma ayesu andipatsa esiteti
Ndikalambire m'chipata lelo wandipereka jubeki
Ndilibe anzanga, lero wandi ninkha network

Sindifuna kugwetsa misozi mabvuto ndipatseko break
Pano ndine osangalala (Am in a happy mood)
Lelo ndine osangalala (Am in a happy mood)

Kunali tsiku ndinalu dyela nkhono
Abanja osacita ngati you don't know
Ma piece work ninalu timba I did more
Lekani lomba ndi mwenthule i do more

Umphawi kulibe ndi partying
Bemuda kulibe ndi ma Jean
Lomba uchi nondo uli mu ma gene
Ami zili kuno, imagine

Ine ndinali kufunako chengelo koma ayesu andipatsa chigayo
Ine ndinali kufunako chengo koma ayesu andipatsa esiteti
Ndikalambire m'chipata lelo wandipereka jubeki
Ndilibe anzanga, lero wandi ninkha network

Sindifuna kugwetsa misozi mabvuto ndipatseko break
Pano ndine osangalala (Am in a happy mood)
Lelo ndine osangalala (Am in a happy mood)
Lelo ndine osangalala (Am in a happy mood)

Am in happy mood, every part we grooving
Ndipatseni chakudya, n'chakumwa futi
Ndi ninkheni vodzidzila
Sini kamba pali vinyu aii sini thila
Kuchoka tsiku ndina sinthila
Kwene mbanje, fodya, aii sin'fiila

Ndi shokeleni mbuzi
Osati ma bulls
Itani ashoes
Aankolo andi bweretsere juice

Ine ndinali kufunako chengelo koma ayesu andipatsa chigayo
Ine ndinali kufunako chengo koma ayesu andipatsa esiteti
Ndikalambire m'chipata lelo wandipereka jubeki
Ndilibe anzanga, lero wandi ninkha network

Sindifuna kugwetsa misozi mabvuto ndipatseko break
Pano ndine osangalala (Am in a happy mood)
Lelo ndine osangalala (Am in a happy mood)
Lelo ndine osangalala (Am in a happy mood)

Credits
Writer(s): Choolwe Siamubotu, Cosmas Fenny, Maxwell Msoni
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link