SHANDANGUZA

Kukunokulilongwe
Osaiwala, pompaja, a Lazy again

Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Mungogona, mungokoka guza
Mukula mopusa
Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Ana ogona
Mungokoka guza
Mukula mopusa

Ngati GABA JEG tandipase shotitu
Kwathu ndi kutalika koma JEG ndi shotitu
Sindifila gin koma ndimenyabe shotitu
Ndimatha kupha beat kuombela zima shotitu
Chi mento chili mwala lazy b achiponde
Sine mwana okulila chiponde
Zaine funsa Steve Chinga mofat
Muvu yanga sia nkhumba yachi more fat
ANangovela GABA mtima wao gugugu
Nangovaya ngati Eli hit ya gugugu
Ine ndinali zoba ku past tu
Pano ndilibe two koloko ndi past two

Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Mungogona, mungokoka guza
Mukula mopusa
Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Ana ogona
Mungokoka guza
Mukula mopusa

Mfana wamfupi kuno ku Lilongwe
Ndithoke ngamo ati ndi chipongwe
Ndili pa level 4 inu nti mabongwe
Musakambe za beef mukudya bonongwe
Olo mdima ugwe
Magetsi ngwe
Ndife ana achikoka popanda zingwe
Mbili inaenda yokha, mpaka ku mpingwe
Amanditcha Mr. Short guy ine ndi igwe

They call me big man, big shot
The Don D D
I do run
Big things with profit
Ku two far Fourner the whole city
Sick man, ine ndi covid

Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Mungogona, mungokoka guza
Mukula mopusa
Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Ana ogona
Mungokoka guza
Mukula mopusa

ANangovela GABA mtima wao gugugu
Nangovaya ngati Eli hit ya gugugu
Ine ndinali zoba ku past tu
Pano ndilibe two koloko ndi past two

They call me big man, big shot
The Don D D
I do run
Big things with profit
Ku two far Fourner the whole city
Sick man, ine ndi covid

Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Mungogona, mungokoka guza
Mukula mopusa
Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Ana ogona
Mungokoka guza
Mukula mopusa
Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Mungogona, mungokoka guza
Mukula mopusa
Ndangobwela, kuza shandanguza
Ndikupusha, ndikugadabuza
Ana ogona
Mungokoka guza
Mukula mopusa



Credits
Writer(s): Joy Gondwe
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link