Mvetsela (feat. Temwah)

Mwana wanga
Ngati umandikonda mvetsela
Mwana wanga ngati umaukonda moyo wako sintha

Ndati palibe palibe palibe
Angakugwile dzanja pamavuto
Ndati palibe palibe palibe
Angakugwile dzanja pamavuto mwanawe

Kamdothi thawa mvula
Kamdothi thawa mvula
Kamdothi thawa mvula
Kamdothi thawa mvula
Kamdothi thawa mvula

Uuuuh mwana wanga mvetsela mvetsela
Uuuuh mwana wanga mvetsela mvetsela

Komabe njoya mosamala poti nkhondo ndi anansi
Amabwela ngati achibale koma mpeni atapanila kuphanzi

Uuuuh mwana wanga mvetsela, mvetsela

Credits
Writer(s): Robert Ching'amba
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link