Mtopola

Ah Hee
Ah Hee
Ah Hee
Yeah hee

Mukukamba zinkhani zambiri
Mukufuna ndiwononge mbiri
Kodi nchikondi
Ndimayesa tilimo awiri
Muli ndi nthawi muli busy
Chonde msachimwise
Ayi nsadanise
Ndi wangayu

Achuluka anthu okhomelela ahahaha
Kankhani pang'ono kupemelela koma why
ATI ndingofuna ndingokudyela ineyo
Atumapo anthu kuzandikwenya ndee
Tinamenyana

Mumvetse
Olo mu dameje dameje
Kumuleka sizingatheke
Ndimadana ndi mtopola
Muleke
Zomakamuwuza miseche
Ndicholinga choti athese
Ndimadana ndi mtopola
Ine ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola
Ndati ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola

Yeah
Umaganiza bwanji kukwatira beast
Iweyo ndi Ka beauty ofunika Prince
Mamuna Oti nthumba anathila yeast
Osati kafinyanya wonunkha gilisi
Mhuu koma mtopola
Ndizamumveso wina nzamunokola
Kumawuza anzake andisomphola
Ndizamponda pamutu ndi chigogoda
Cell nzalowa Bola ndamtchola
Eya pezani zina zochita
Eya kupeza wanu nzovuta
Eya mungomupempha Chauta
Osativuta

Mwachuluka anthu okhomelela
Kankhani pang'ono kupemelela
ATI ndingofuna ndingomudyela
Koma tizamenyana

Mumvetse
Olo mu dameje dameje
Kumuleka sizingatheke
Ndimadana ndi mtopola
Muleke
Zomakamuwuza miseche
Ndicholinga choti athese
Ndimadana ndi mtopola
Ine ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola
Ndati ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola

Olo mu dameje dameje
Kumuleka sizingatheke
Olo mumuwuze miseche
Yeah ey yeah
Yeah ey yeah
Ndimadana ndi mtopola

Mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola
Ndati ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola

Mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola
Mtopola eh mtopola
Mtopola eh mtopola
Ndimadana ndi mtopola



Credits
Writer(s): Joy Gondwe
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link