Zonse Zanga (feat. Mastol)

Yeah
Ndili wamasiye munakhala kholo
Kusiya ulemelero kusankha kapolo
Mwayankha mafunso opanda ansala olo
Ntakumana ndi zokhoma muzakhalapo
Poti ndinu amene munandilipilira dipo
Mutaponde phazipo nane ndipondepo
Mundigwire mkono musandisiye ndipo
Ndikhale nanu closer ngati John, Peter ndi Paul
Mukanena "muka" ndizigalamuka
Kunka kukalalika mukangolamula dzuka
Ine pompo osalefuka
Mukati nyamuka
Monga wopolumuka sindikopeka n'kutchuka
Ku mliri wosakaza napempha mundionjole
Mwamva nkhawa zanga ndisanalongosole
Heh, simunalole
Mdani andikole
Mbuye mwandisuntha from glory to glory

M'mene mwayandikira
Chikho chasefukira
Moyo wanga unasintha
Mtima wanga kuyamika
Ndizovuta kunena
M'mene m'mandikondera
Mwandimasula ku nsinga
Mtima wanga kuyamika

Ndinu zonse zanga
Zonse zanga whoa
Zonse zanga
Zonse zanga whoa
Ndinu zonse

I could have been lost, yes, a hot mess
Or maybe with no breath, or so stressed
But you've given me no less than more blessings
I'm predestined for conquest I confess it
Ah
And you know me, oh
You don't keep accounts of the old me, oh yeah
Zitseko zomwe mwatsegula
Madzi odikha kundimwetsa olo wina amange mvula
Oh I can't believe Your love came for me
You're like taste and see, all by faith receive
And I'm like how can it be that a person like me is taken to be
A vessel of peace and eternally free?
It's crazy but sweet
Sindingayiwale, I remember yeah
Simungandithawe sindili ndekha, sindili - ah
Lord you saved me and I'm free
You are everything to me yeah yeah

M'mene mwayandikira
Chikho chasefukira
Moyo wanga unasintha
Mtima wanga kuyamika
Ndizovuta kunena
M'mene m'mandikondera
Mwandimasula ku nsinga
Mtima wanga kuyamika

Ndinu zonse zanga
Zonse zanga whoa
Zonse zanga
Zonse zanga whoa
Zonse zanga
Zonse zanga whoa
Zonse zanga
Zonse zanga whoa



Credits
Writer(s): Masa Topola
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link