Khala (feat. Viddiex fyah & Joe Ikon)

Uli ndi mbuyo yokukhala!
Osakhala kutali pamiyendo panga khala!
Lelo we're gonna dance while seated khala!
Khala khala khala!
Khala!
Lelo palibe akagone kwawo

Defender!
Mwanakazi iwe nde utipweteka
Fashion killer trend setter
Pa akazi Onse ndingowona iwe wekha
Umamva Bwanji?
Way your booty bounce ngati njanji
Pa iwe ndagoma
Sindikathe kutakata no mitaji
Yuh mi chargie
We're gonna get high while low
Lap pon di throne as you whine slow

Uli ndi mbuyo yokukhala!
Osakhala kutali pamiyendo panga khala!
Lelo we're gonna dance while seated khala!
Khala khala khala!
Khala!
Lelo palibe akagone kwawo

Ndakuona ntangofika
Ine nkufila pompo kuima
Ka dress katakugwila
Mokusisita
Ngati lochita
Kusokela pathupi pompo oh
Ine kuzizidwa munkhongono
Apa ndiona maso ankhono
Koma singathe kudekha
Kudekha dekha so
We're gonna get high while low
Lap pon di throne as you whine slow

Uli ndi mbuyo yokukhala!
Osakhala kutali pamiyendo panga khala!
Lelo we're gonna dance while seated khala!
Khala khala khala!
Khala!
Lelo palibe akagone kwawo

Uli ndi mbuyo yokukhala!
Osakhala kutali pamiyendo panga khala!
Lelo we're gonna dance while seated khala!
Khala khala khala!
Khala!
Lelo palibe akagone kwawo



Credits
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link