KUKOPELA. - remix

Ku ding dong aliko Ku ghetto alikoso
Ku ntchito aliko ma copy cut ayi nono
This is the remix we don't take it easy
This is the remix
Madness we the baddest baddest let's go

Ukayamba geni ma guy akubwela ati nafeso
Moyo okopela pamalawi wanyanya tisanamepo
Ndikavalabo kutchena afuna avaleko
Chinawatsalila mchiwanda chowonela mayeso
Kopela chilichose kopela
Akangoonela chilichose kopela
Kopela chilichose kopela
Akangoonela chilichose kopela

Look what I did for my People in Transkei
Thati Xhosa Rap from Capetown to Blantyre
Ndisphana ndzima Tryna Raise Flag High
Kodwa BombaKlyde wanna move like I did
Tryna Walk in these shoes and its my Feet
Ingxaki yam I yam I wanted all of us to Win
Ungandbuzi ndenze Njani God Did
Ngenxa yomona yo'll tried kill my Dream
Why u hate I n I
Numi ngiPhume kasi I thought you'd wanna see me Shine
Sgaphikisani this is my time
Bhudda of the Year made Xhosa Rap Fly!
Ndithi Abanye Bayakhopelaaa
And Bona Fostelaaa
NdiyaKhumbula BesBomonela
Basbona swinaa bayaSondela

Mpaka Akukopela kotenga ngongole
Kodi mwakongolako Tipeza munthu
Mm achimwene Nafe Tizitapee Ntchito ya mutu ndikudyelapo Masuku Paja
Ndadabwa Adhawa Kwatsalaku Cash adzaipanga Photocopy
Mm Sinanga Sagwila money Ife timaigwila Ngati 0-40
Ndikahopela nkazi Nawo Akuhopela
Ndikalowelela Nawoso Akusochela
Ukati ukhwefule nawo akukhwefula
Usakhwefule nawo Troggi akukokela
Chabwino ndingoyamba Geni ndipange ndalama koma

Ukayamba geni ma guy akubwela ati nafeso
Moyo okopela pamalawi wanyanya tisanamepo
Ndikavalabo kutchena afuna avaleko
Chinawatsalila mchiwanda chowonela mayeso
Kopela chilichose kopela
Akangoonela chilichose kopela
Kopela chilichose kopela
Akangoonela chilichose kopela

Akubela man Davie afuna awafile Madonna
Chilichonse photocopy I think waachulukila tonner
Anzao akuphanda iwo akubanda ku mpanda
Akuti ma stonner
Nzao uja wasiya geli nawonso asiya nao, koma boys sizoona
A kujaiva ngini yoti siyawo
Anadaiva ref caller foul
Akuliva ghetto kubela ding dong
Lero ndiize awathamangitsa kwao
Control C Control V
Funa kubela Genna from 18B
Don't play with yo future anzanu mukubela wo Makolo awo ali ndi plan B
Di world ah full ah bad people
Dem no like fi see di Ras ah drive vehicle
Ah nuff ah Dem ah evil
No wan see mi rise to ah higher level
Ah dem just can't let me Bee nao afuna akhale Njuchi
Zonse zabwino akhale Ndiwo Ali Msuzi
Ndikangodya pause nao anvekere tchuzi
Angotengera zilizonse mpaka atenga Edzi
Sting dem hard man ah copier fire burn
Sungandiwalire u can't copy di sun
Kunvetsa chison musamachite makan
Popanda likasa ndinu ma zero pa ten
Ah we burn di fire
Iwo amangopala
Ah we burn di fire
Iwo amangopala

Ukayamba geni ma guy akubwela ati nafeso
Moyo okopela pamalawi wanyanya tisanamepo
Ndikavalabo kutchena afuna avaleko
Chinawatsalila mchiwanda chowonela mayeso
Kopela chilichose kopela
Akangoonela chilichose kopela
Kopela chilichose kopela
Akangoonela chilichose kopela



Credits
Writer(s): Madalitso Kantema
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link