Vuto Ndichani

It's that money making music

Ndalama zikandiyanja sindimasowa
Ndimapenga nazo, ndimapenga nazo
Ndalama zikandiyanja sindimasowa
Ndimapenga nazo, ndimapenga nazo

Tandigwile, tandigwile, happiness mbwe mbwe mbwe
Tandigwile, tandigwile ine, happiness mbwe mbwe mbwe

Happiness mbwe mbwe mbwe, happiness mbwe mbwe mbwe

Zochepa ndili nazo zimandikwanila
Zochepa ndili nazo zimandikwanila
Zochepa ndili nazo zimandikwanila
Zochepa ndili nazo zimandikwanila

Vuto ndichani, ndalama zanga, kumandinena tandiuzeni

Iiiiiiiih iiiiiyaaaa hiii hiii
Iiiiiiiih yaaaa hiiiiiyaa ah
Iiiiiiiih iiiiiyaaaa iiiya iyaaa ah hii hii hii hii
Iiiiiiiih iiiiiyaaaa iiiyaaaa aaa aaaah

Anthu otani mumakondwela
Zikamavuta mumakondwela
Basi nkhani kundipekela, mwati uyu sizimuyendela

Credits
Writer(s): Temwah Gondwe
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link