Arasi

Yeh yeh
Yeaah yeaah
Yeh yeh yeh yeh yeah
Yeaah yeaah

Ife ndi Mafana oti basi
Ndukuuzani arasi
Zofuna zathu sizambiri
Mufuna chani?
Malawi gin basi
Ukafuna ukatipeza ku show
Pakhomo zingati?
Five pin basi
Carina ya m'dala tasiya pa mbowee
Abraz tikwera minibus
Ife ndi Mafana oti basi
Ndukuuzani arasi
Zofuna zathu sizambiri
Mufuna chani?
Malawi gin basi
Ukafuna ukatipeza ku show
Pakhomo zingati?
Five pin basi
Ife ndimafana oti ah huh
Ife ndimafana oti basi

Akafunsa wakutuma ndi Malinga
Nyama kuseli tikuzinga
You is a Vegan eko zikapinga
Me juss dribble inna di middle Camavinga mmmh
Mafana bwanji mufuna kumandipinga
Kundiyenda ngati njoka mukapinga
Mu njale mwanga mwangodzadza dzima singer
Ukafuna cross crew yonse ndima winger ah huh

Ife ndi Mafana oti basi
Ndukuuzani arasi
Zofuna zathu sizambiri
Mufuna chani?
Malawi gin basi
Ukafuna ukatipeza ku show
Pakhomo zingati?
Five pin basi
Ife ndimafana oti ah huh
Ife ndimafana oti basi

Zima bouncer kuseli kudya bench
Mkazi wa malonda timukhomela bench
Sober man lero nde akhuta quench
Bar man ndamuuza keep change
Martse ananena kale loud and clear
Kupatula mkazi wanga chomwe ndimakonda ndi beer
Kuyenda ndi ma tradi kumwela kwa TA
Amene takonzeka tiyeni
King size Lizzla ndiyemwe ndikusut'la
Zima mamie kufupi zungosunth'la
Ma style ndungosintha kamas'tla
Pa counter ma shot tungoshu'tla

Ife ndi Mafana oti basi
Ndukuuzani arasi
Zofuna zathu ndizambiri ngati?
Njee
Malawi gin basi
Mu kafuna mukatipeza ku show
Pakhomo zingati?
Five pin basi
Ife ndimafana oti... ah huh

Ife ndimafana oti basi
Ife ndi Mafana oti basi
Ndukuuzani arasi
Zofuna zathu sizambiri
Mufuna chani?
Malawi gin basi
Ukafuna ukatipeza ku show
Pakhomo zingati?
Five pin basi
Ife ndimafana oti... ah huh
Ife ndimafana oti basi



Credits
Writer(s): Chikumbutso Banda
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link