Abale Anga (feat. Macelba)
Blood is thicker than water
Family is all that matter
I'll always love you harder indee
Ndinu abale anga inu
Ndinu abale anga inu
Munadusa pokhala anzanga inu
Mumaukomesa moyo wanga inu
Agulu langa inu
Olo tisemphane simundituluka
Olo ndikunyozeni mumakhululuka
Inde kusemphana sikumalephelera
Mu umodzi muli mphavu abale kumandipemphelera
Family is supposed to be supportive
No negative vibe all love
Family is a bond made on earth and above
If family is like a pool then let us all dive
Let us all dive
Nde osamadana osajedana
Kumakondana pachibale osaphana
Chibale ndi chipyela sumangogwela
Umodzi usathe Kholo kumawamvela
Zikalakwika kumauzana chonde
Tizachita bwino ngati nthaka ya chonde
Ka get together bwa? Tikacheze pakhonde
Kuli matenda, tiyeni tonse tikazonde
Ndinu abale anga inu
Ndinu abale anga inu
Munadusa pokhala anzanga inu
Mumaukomesa moyo wanga inu
Agulu langa inu
Ndikawina
Nanuso!
Ndikagula Njale
Njanuso!
Ndikamanga Den
Nkwanuso!
Olo ndikapeza Nkazi
Mmmh mmmh
Chibale chipyela
Tingasemphane chilibe pothela
Tingatulukane kukonda adela
Ndizathamangila Iwe vuto likandigwela
Mmmh you are my blood O+
If I got ill no fuss
Pena ndiwe poison pena ndiwe charm
Walter Nyamilandu I'm just stuck with FAM
Nditha kukhala mwezi osakukhola
Chibale sichimatha osachitola
Kapena osachitaya
Zima day ones osazitaya
Blood is thicker than water
Family is all that matter
I'll always love you harder indee
Ndinu abale anga inu
Ndinu abale anga inu
Munadusa pokhala anzanga inu
Mumaukomesa moyo wanga inu
Agulu langa inu
Ndinu abale anga inu
Family is all that matter
I'll always love you harder indee
Ndinu abale anga inu
Ndinu abale anga inu
Munadusa pokhala anzanga inu
Mumaukomesa moyo wanga inu
Agulu langa inu
Olo tisemphane simundituluka
Olo ndikunyozeni mumakhululuka
Inde kusemphana sikumalephelera
Mu umodzi muli mphavu abale kumandipemphelera
Family is supposed to be supportive
No negative vibe all love
Family is a bond made on earth and above
If family is like a pool then let us all dive
Let us all dive
Nde osamadana osajedana
Kumakondana pachibale osaphana
Chibale ndi chipyela sumangogwela
Umodzi usathe Kholo kumawamvela
Zikalakwika kumauzana chonde
Tizachita bwino ngati nthaka ya chonde
Ka get together bwa? Tikacheze pakhonde
Kuli matenda, tiyeni tonse tikazonde
Ndinu abale anga inu
Ndinu abale anga inu
Munadusa pokhala anzanga inu
Mumaukomesa moyo wanga inu
Agulu langa inu
Ndikawina
Nanuso!
Ndikagula Njale
Njanuso!
Ndikamanga Den
Nkwanuso!
Olo ndikapeza Nkazi
Mmmh mmmh
Chibale chipyela
Tingasemphane chilibe pothela
Tingatulukane kukonda adela
Ndizathamangila Iwe vuto likandigwela
Mmmh you are my blood O+
If I got ill no fuss
Pena ndiwe poison pena ndiwe charm
Walter Nyamilandu I'm just stuck with FAM
Nditha kukhala mwezi osakukhola
Chibale sichimatha osachitola
Kapena osachitaya
Zima day ones osazitaya
Blood is thicker than water
Family is all that matter
I'll always love you harder indee
Ndinu abale anga inu
Ndinu abale anga inu
Munadusa pokhala anzanga inu
Mumaukomesa moyo wanga inu
Agulu langa inu
Ndinu abale anga inu
Credits
Writer(s): Smart Banda
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Link
© 2025 All rights reserved. Rockol.com S.r.l. Website image policy
Rockol
- Rockol only uses images and photos made available for promotional purposes (“for press use”) by record companies, artist managements and p.r. agencies.
- Said images are used to exert a right to report and a finality of the criticism, in a degraded mode compliant to copyright laws, and exclusively inclosed in our own informative content.
- Only non-exclusive images addressed to newspaper use and, in general, copyright-free are accepted.
- Live photos are published when licensed by photographers whose copyright is quoted.
- Rockol is available to pay the right holder a fair fee should a published image’s author be unknown at the time of publishing.
Feedback
Please immediately report the presence of images possibly not compliant with the above cases so as to quickly verify an improper use: where confirmed, we would immediately proceed to their removal.