Basi

Ngati ukufuna tikondane tikondane nde pamenepo Basi
Ngati Ukufuna kuti ndikhale waiwe iwe waine nde pamenepo Basi
Pamenepo Basi
Basi
Basi
Basi
Pamenepo Basi
Auze ansanje akagwere kutali
Iwe ndi ine nde pamenepo Basi

I ain't going anywhere
Loving you all the way
Maso anathera ndikufela pa iwe
Sit down Mamie
I know kocheza umamva nkhani
Fanzi kufuna kukusinthitsa plan
Koma ine ndekha am your Man
Mamie
Chete kubanja Basi
Kupanikizika ndi nthanzi Basi
Chikondi chokha chokha Basi
Iwe wekha ndizakhetsera Gazi
Never stress
This good loving just embrace
What a blessing
Yeah

Koma Ngati ukufuna tikondane tikondane nde pamenepo Basi
Ngati Ukufuna kuti ndikhale waiwe iwe waine nde pamenepo Basi
Pamenepo Basi
Basi
Basi
Basi
Pamenepo Basi
Auze ansanje akagwere kutali
Iwe ndi ine nde pamenepo Basi

Yeah
Ndimadziwa that you talk to them people
And they keep telling you we ain't equal
Umadziwa chani ili ndi dziko
Anthu akakuona mwamba amafuna utatsika
We don't have to worry
As long as you love me
Will you be there for me?
Ngati udzakhalepo pamenepo Basi
Tikubola kunthanzi
Chikondi ndi plus
Nde tatiye Ku Dance
Usamamve za anthu boola makutu
Zikalowa uku kutulukira uku
I need you
I can never lie
I need you each and every second

Koma Ngati ukufuna tikondane tikondane nde pamenepo Basi
Ngati Ukufuna kuti ndikhale waiwe iwe waine nde pamenepo Basi
Pamenepo Basi
Basi
Basi
Basi
Pamenepo Basi
Auze ansanje akagwere kutali

Koma
Ngati ukufuna tikondane tikondane nde pamenepo Basi
Ngati Ukufuna kuti ndikhale waiwe iwe waine nde pamenepo Basi
Pamenepo Basi
Basi
Basi
Basi
Pamenepo Basi
Auze ansanje akagwere kutali
Iwe ndi ine nde pamenepo Basi

Credits
Writer(s): Benjamin Maulidi
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link