I'll wait on you - Official Audio

I'll wait on you
(Yeah)
Zamar Music
C-
(Roar)
L-
(Eh)
Touch

Tonsefe ndife anthu
(Yeah)
Takumana ndi zokhoma
(Ndizokhoma)
Kuluza okondedwa athu
I know the pain
Sizoona
(Sizoona)
Zonsezi Ambuye mumaona
Mavuto omwe sakuchoka
(Sakuchoka)
Tathedwa Nzeuru mitu sikukoka
(Yeah)
You remain God

Chifukwa ndinu nokha ambuye
(Take me higher)
Chifukwa ndinu nokha ambuye
(Yeah, ndinu nokha Ambuye, ndinunokha Ambuye eh)
Chifukwa ndinu nokha ambuye
(Palibe ofana nanu)
Ndinu nokha ambuye
(Palibe ofana nanu I'll wait)

I'll wait on you
(Yes I'll wait)
I'll wait on you
(Mavuto achuluke bwanji ineyo)
I'll wait on you
(I know, I know sizingathe but still)
Wait on you
Yeah Lord
(Yeah Lord)

Zamar
Chibwenzi Chatha
Banja latha
Zonse zatha
Kunja kwada
Kwandidera
Kwandidera
My brother my sister
Hold on
You are too young to die
Please don't don't kill yourself yeah
Oh no oh oh
Osadanda Yesu adzakugwira pa nkono
Nkono
Kunja kudzakuchera
Kudzakuchera

Usaziphe
(Ayi Ayi yeah eh eh)
Usadziphe
(Osayesa Kuchotsa moyo)
Usadziphe eh eh eh
(Ukangolangika za zii)
Usadziphe

(Osadanda Yesu Akugwira)
Usadziphe
(Akugwira, Yesu Akugwira)
Usadziphe
(Mavuto akule bwanji)
Usadziphe
(Ih ih yeah yeh eh yeh eh)
Usadziphe

(Ayi ih ih ih ih ih ih ih)
Usadziphe
(Ayi, Ayi ihi ih ih)
Usadziphe
(Mavuto angachuluke bwanji)
Usadziphe
(Osayesa)
Usadziphe

(Tsogolo ndi lowala)
USadziphe
(Ndi lowala)
Usadziphe
(Osadanda Yesu Adzakugwira)
Usadziphe
(Pa nkono nkono nkono)
Usadziphe
(Eh eh eh, Eh eh eh ih eh ih eh ih eh)

Touch



Credits
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link