I. O. U

Ndimanyadila kuti ndiwe oyamba
Ndipo ndi pemphero ndi pembedzero
Kuti Mulungu adzikupasani zosowa zanu
Apitilize zimene wayamba kale kuchita
Kuti moyo wanu upitebe
Pitilizani kulemekeza komanso kukonda wina aliyense

Hi Mom
I wanna give you your flowers
I haven't been home
I've been working for hours
You believed in me when I didn't
Gave me everything when I need it
You told me one day you will make it
I want to pay you back when I make it
Dear Susan
Mwandisamalira every season
Loving me without a reason
I'm really worried you are getting older and older
Christina
Thank you for giving me my mother
Thank you for being my grand mama
I don't take you for granted

I owe you
I owe you
Mukanawelenga zonse mwandichitira
Ngongole yaikulu yovuta kubwenzela
I owe you
I owe you

If you were counting everything you did for me
I would owe you the world
Life doesn't come with a manual
It comes with a father who loves you and proud
Mukati mulibe ndinkati mukunama
Kusamalira tonse kumaliza ndalama
Ndikazaiphula muzayendela hammer
Ndimakukondani Fadaa
I may not be so perfect
I know it
I'm closer to your heart no regret
Number one fan mwana wathu amaimba
Ndizikonda school osati kuimba
Kulakwa Mayeso a 4
Kumudzi kubweleza 4
You picked me up when I fall
Makolo kusangalala, kukhonza mayeso
Kunditenga ku Mzuni, Degree ndiyanu

I owe you
I owe you
Mukanawelenga zonse mwandichitira
Ngongole yaikulu yovuta kubwenzela
I owe you
I owe you

Popeza Baibulo limatitsimikizila kuti lamulo lalikulu ndi chikondi
Ineyo i'm wishing you well
Pachinachilichonse
Chimene ukupanga
And ineyo i've been there for you always despite whatever things
Komabe kukacha mamawa ndimakupemphelerani
Kuti ngakhale ana anga pakhomo pano palibe
Ali muma school mukhale nawo



Credits
Writer(s): Dan Tadala Kasinjeni, Praise Umali
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link