MWANTINTI (feat. Teddy Makadi & Pon G)

Yeah
It's Only Entertainment
Wole
Wala
Yeah
Very Good Very Good

Kukukisa pang'ono ngati ka 2par
Unati ndisamasuke kwanu ndi koshupha
Ndikafika pa gate n'salize hooter
Ndizingolemba message mpanda uziwudumpha
Pena pake ndiwe ka mkazi kofuntha
Zomwe tikupangazi akwanu azandikuntha
Alibe nazo zoti ndine wotchuka
Zoti ndimaoneka pa TV pa Luntha

Ndi ka light skin girl ngati Amarula
Body lining sanayuze ruler
Love language yake nnati dollar
Ine mayine koma sindilola
Let me take you to Munalula
You rob my heart ndiwe kawalala
Mmangofuna uzisangalala
Ma love obhebha ngati za mankhwala

Mmh love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)
Mmh I love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)
Mmh I love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)
Mmh I love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)

Zikukoma ngati nyama yakufupa
Battery la moyo wanga lafika pa full bar
Koma kwanu ati ndine kape ndine luga
Amandionera diso limodzi la Ruger
I'm gonna represent you though I ain't passed the bar
Baby girl I gotchu we gonna go far
Ngati Bluetooth devices tinalinka
Mami ndinu chida ndinu kilinka

Sumasunga tu ma secret mayine secret
Zimandiwaza zopita ku ma picnic
Tiye kunyanja ndikayiphula ticket
Na iwe ndi ndi ndikumata ti
Ati Chikondi ndi mbo
Kondi ndi mbola
Kwa iyeyo bola ndimpatse zi dollar
Komabe ine love yako nde ndiyitola
Strictly lobola ndiyomwe uyiwona

Mmh love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)
Mmh I love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)
Mmh I love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)
Mmh I love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)

Uzipola moto ukamandithoka
Uchepetse za mavuvu siwe motorcar
Zomwe ndimafuna utsanzike pochoka
Nsanje zayamba kuchuluka mtima utchoka
Ndisaone kakape ka kukuthoka
Sindisekelera kakaka zopotoka
Ukafuna dollar trans ID kuti kha
Usamaope kupititsidwa ku chatinkha
Mkaziyu ndi wanga wa ine ndekha
Sitimaitana gulu potenga chindekha
Ndikati ndikugwa amandiwakha
Uyu nde ndimanyadila kuti ndinasankha
Very Good

Ndikumva tseketseke ngati sugar (Illovo)
Ngati kumaloto (Loto)
Hunnie!
You're my Princess
Kukonda iwe sindipanga regret

Mmh love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)
Mmh I love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)
Mmh I love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)
Mmh I love you more (bebi)
Mmh I love you mwantinti (bebi)



Credits
Writer(s): Noel Phyzix Chikoleka
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link