Attention (feat. Indonga)

Ndili mu chikondi ndiiwe
Osati chifukwa cha ndalama
Ine ndili mumtima mwako
Chifukwa ndikufuna chikondi

Ukachoka ndimadwala ndimakusowa uli pompa
Kuika chimwemwe mumtima mwanga iwe
Ukachoka ndimadwala ndimakusowa uli pompa
Kuika chimwemwe mumtima mwanga iwe

Zoona imwe mukhala busy koma musamaiwaleko ka lamya
Olo kutuma ka message imwe
Honey kodi waswera bwanji
Tsiku likuyenda bwanji
Ine mumtima mwanga nimva bwino eh eh ah

Nimvera bwino (ah ine)
Baby nimvera bwino (muntima mwangamu)
Newo nimvera bwino (ah ine)
Ine nimvera bwino (muntima mwangamu)
(Ineyo) siine ovuta (ayo)
Nifuna chabe ka attention
(Ineyo) siine wa Nsanje
Usandimane nthawi yako
(Ineyo) siine ovuta
Nifuna chabe ka attention
(Ineyo) siine wa nsanje (mmh)
Usandimane nthawi yako

Ena ati amuna ndi agalu
Ena ati mamuna ndi pamimba
Ena ati mamuna ndi mwana
Koma ine ndikutchula moyo wanga ndiwe

Poti ukachoka ndimadwala
Ndimakusowa uli pompo
Kuika chimwemwe mumtima mwanga
Poti ukachokapo ndimadwala
Ndimakusowa uli pompo
Ndikufuna iwe pamoyo wanga

Pena inde mukhala busy (busy)
Musamaiwaleko ka phone (phone)
Pena kutuma ka message imwe
Honey kodi mulibwanji ine kuntchito kuno nakusowani
Mumtima mwanga ndimvera bwino inewo oh

Nimvera bwino (ah ine)
Baby nimvera bwino (muntima mwangamu)
Newo nimvera bwino (ah ine)
Ine nimvera bwino (muntima mwangamu)
(Inewo) siine ovuta (nonononono)
Nifuna chabe ka attention
Siine wa Nsanje
Usandimane nthawi yako
(Ineyo) siine ovuta
Nifuna chabe ka attention
Siine wa nsanje
Usandimane nthawi yako

Nimvera bwino (ah ine)
Baby nimvera bwino (muntima mwangamu)
Newo nimvera bwino (ah ine)
Ine nimvera bwino (muntima mwangamu)
(Inewo) siine ovuta (nonononoo)
Nifuna chabe ka attention
Siine wa Nsanje
Usandimane nthawi yako
Siine ovuta
Nifuna chabe ka attention
Siine wa nsanje
Usandimane nthawi yako



Credits
Writer(s): Enort Spear Mbandambanda, Indonga
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link