Prayer

Issy teni pawa
Go

Ndifuna kupha thupi ine bububu
Mabvuto akabwera what do you do
Uzakhala phe mtima gugugu
Mwina uza uza ambuye Yesu heal me
Too
Ndifuna kupha thupi ine bububu
Bvuto ikabwera what do you do
Uzakhala phe mtima gugugu
Mwina uza uza ambuye Yesu heal me
Too
Pemphe pemphe pemphera
Pemphe pemphe pemphera
Pemphe pemphe pemphera
Pemphe mwana wangu pemphera

I got a lot of things aise I owe to God
Nthawi zina ndimakhala oputsa and
Still He got my back yea
Ndimagwa kugonjetsedwa and back ku
Ciyambi
And I always promise not to double
Cross you ngati miyambi
I won't do it again, conde ndipatseni
Ujeni
Kuti ndi chimwe n'funseni, che china
Lenga n'chiteni
You've faithful inu Yesu niwalitseni ngati
Khafu
Nine chiphwafu ngati thafu
Olo anthu andi'ona nyafunyafu
Huh mukuti I'm a diamond in the dirt
Creatively orchestrated masterpiece
You see instead
The corner stone the builder rejected
You belt a church instead
Wanna work and be fruitful for you
Water me here's a bed

Ndifuna kupha thupi ine bububu
Mabvuto akabwera what do you do
Uzakhala phe mtima gugugu
Mwina uza uza ambuye Yesu heal me
Too
Ndifuna kupha thupi ine bububu
Bvuto akabwera what do you do
Uzakhala phe mtima gugugu
Mwina uza uza ambuye Yesu heal me
Too
Pemphe pemphe pemphera
Pemphe pemphe pemphera
Pemphe pemphe pemphera
Pemphe mwana wangu pemphera

I live in a space were temptations
Everyday
Umoyo nika journey n'kumva njota day
By day
I really wanna change this
M'bongo mwanga erase this
Mafupa reset this
All the demons Uhh chase this
Aise ndimayesa lomba how to do it
Mapemphero ndalema ku pempha
Mwina n'kuwe
Anzanga ndi tech wanna make it seem
Eyy
Ngati iwowa ali ndi golide ineyo nguwe
I long to hear your voice, calm the storm
And just take it all
Yehovah simupenya nkhope posintha
Mibo
Nkongole zanga ninali nazo I heard you
Paid it all
Ndagwada pama phadzi panu Ayesu
Make me whole

Ndifuna kupha thupi ine bububu
Mabvuto akabwera what do you do
Uzakhala phe mtima gugugu
Mwina uza uza ambuye Yesu heal me
Too
Ndifuna kupha thupi ine bububu
Bvuto ikabwera what do you do
Uzakhala phe mtima gugugu
Mwina uza uza ambuye Yesu heal me
Too
Pemphe pemphe pemphera
Pemphe pemphe pemphera
Pemphe pemphe pemphera
Pemphe mwana wangu pemphera



Credits
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link