Themba Ndi Themba

Themba themba themba themba themba
Themba
Amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
Anangodabwa tangofika ndikubhebha
Trap yathu sungalowe fukwa siwe member
Iyi ndi ya ma shatter ndi themba ndi themba
Amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
Anangodabwa tangofika ndikubhebha
Trap yathu sungalowe fukwa siwe member
Iyi ndi ya ma dada ndi themba ndi themba
Themba ndi shatter themba ndi Don dada
Themba ulemu amalandila ku Lusaka
Amamufila mu ghetto anthu amamutsata
Mumapusisana mukamati Samatha
Themba padeni amamutchula mbwindi
Themba mkazi wake ndi wophula ndi chi biggie
Themba ndi wachifumu koma samadya kings
Themba ghetto inamudya kma looks ya dings
Tikufuna themba tikufuna drip
Ukaona themba ndekuti waona cheese
Themba ndi good boy themba ndi wamu street
Themba boys yake siyizamva ayi
Mmm mm
Themba themba themba ndi big stepper
Themba themba themba ndi big dripper
Mukapanga za themba mutsegula mmimba
Mukafuse mbali za kwanu themba amamuziwa
Themba ndi wachilokolo koma amaziwa stuff
Sungamuyike mu botolo themba ndi wamakani
Themba be the reason mkazi wako sakuyankha
Machesi Ali ndi ife nde themba amangoyaka
Mmm mm
Boys yake siyizamva,ayi
Themba anachosa mantha, wallahi
Themba ndi chi uchi
Themba si chi mphwepa
Themba sanena odi kwanu tizagenda
Amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
Anangodabwa tangofika ndikubhebha
Trap yathu sungalowe fukwa siwe member
Iyi ndi ya ma shatter ndi themba ndi themba
Amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
Anangodabwa tangofika ndikubhebha
Trap yathu sungalowe fukwa siwe member
Iyi ndi ya ma dada ndi themba ndi themba



Credits
Writer(s): Themba Kasambara, Themba Mhango
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link