Step by Step

Hahahaha
Malawian,Yeah
It's That Time You know mmmh
Step by Step tikukwera wekha ukuona kuti tikupanga Elavate
Ma Guy nde Asankha kuti azifila Spe
Nde ena akuopa akupanga Hate
Sleepless Nights Saku Gona
Asapezeke pa Poster
Aka Runner Ting sitingamupeze
Utha kuma Heta
Koma Sungandilese
Utha kuma heta
Koma sungandilese
Fresh and Clean pa chi Corner
Kumata po Poster
Show Yo Runner Ndekha
Home Boys Tsitsi wango pota
Tonse Tangotchena Ndani amati Tikupenga?
Ndine One Of a Kind ngati Ganja
Iweyo Tangodekha
Olo abwere ndiyolenga
Aliyense apa anayamba Yekha
Sitinayambile limodz
Ngati Liwiro la Mu mchenga
From zigege To Tacos
Ndichi fine mami ngati Riana Bagus
Ndinayambira Kusuta Mibongo
Pano 1 par yokha imazunguza Ubongo(okay?)
1pa yokha itha kuzunguza ubongo
1pa yokha imazazunguza ubongo
1pa yokha itha kuzunguza ubongo
Wamva,Step by Step tikukwera
Wekha ukuona
Kuti tikupanga Elavate
Ma Guy nde Asankha kuti azifila Spe
Nde ena akuopa akupanga Hate
Sleepless Nights Saku Gona
Asapezeke pa Poster
Aka Runner Ting sitingamupeze
Utha kuma Heta
Koma Sungandilese
Utha Kuma Heta
Koma Sungandilese



Credits
Writer(s): Chifundo Chingaipe
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link