Bwenzi Zikoma

Yeah
ChaPo
Yeah yeah

M'tima uli phee
Ozaza ndi chimwemwe eh
I call you my babe
You call me your baby eh
Get close to me babe
Tabwera usendeze eh
Leave no space between us
Ansanje
Tisawapase mpata

Coz' you know
I know
How it goes from here
You go where I go
We elope from here
Vama love izi
Ati you can die
Vama love izi
Ndizokoma

Zimatele zimatele (tele tele tele tele)
Bwenzi zikoma
Zimatele zimatele (tele tele tele tele)
Bwenzi zikoma
Iwe ndi ine (Zikoma)
Kukondana (Bwenzi zikoma)
You and i
Ziko ziko ziko bwenzi zikoma

Mmm chabwino timayambana
Posanvesetsana kukangana
Koma timakhulukililana
Mmm kukondana
Kupemphelelana
Mwa Ambuye timapambana
Tikafooka timakankhana
Mbambadi mpaka banja

Coz' you know
I know
Where it goes from here
You go where I go
We elope from here
Vama love izi
Ati you can die
Vama love izi
Ndizokoma

Zimatele zimatele (tele tele tele tele)
Bwenzi zikoma
Zimatele zimatele (tele tele tele tele)
Bwenzi zikoma
Iwe ndi ine (Zikoma)
Kukondana (Bwenzi zikoma)
You and i
Ziko ziko ziko bwenzi zikoma

Zikoma bwenzi zikoma
Zikoma bwenzi zikoma
Ziko ziko ziko bwenzi zikoma
Zikoma bwenzi zikoma



Credits
Writer(s): Charles Ponderani
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link