BONA
Yahman yah
Tellem
Zomwe ndikumaona
Dziko li linagona
Satana Pano anangolowa paliponse kulimeza ngati chi Ng'ona
Akufalitsa ti mabodza
Angofuna kuti pomboneza
Eti uthenga wabho ena ati ndizanyasi mhhu mukumanyoza ah ah
Koma sindingasiye Ku praiser ine praiser ine eh
Ndimamutsata Yahweh ndipo ndimamupembeza ine mbeza ine hey
Masten aziziwa mawu awo mawasungabe sungabe eh
Uzikonda Chauta
Namalenga pokusunga iwe sunga iwe hey
Devil yo kumubona ahah
Mpaka akumagoma ahah
Wakumana ndi CHIPHONA ah
SUNDIKOPA kopa ase
Devil yo kumubona mmhu
Mpaka akumagoma mmhu
Wakumana ndi CHIPHONA
SUNDIKOPA kopa ase
Ey yeah yah
Ndipo sinkuopa ase
Ey yeeh yah
SUNDIKOPA kopa ase
Ey yeah yah
Ndipo sinkuopa ase
Ey yeah yah
Kuyimba nako kukayamba kukoma
Satana naye nde saku mapuma
Akusaka tinjira atikole tizimupopa koma wagoma
Nyengo zaka nazo zikayamba kusintha
Ndipamene akufuna ndizifuntha
Kenako nkhale desperate ndimutsate eti sindipanga izi ataaa

Devil yo kumubona ah ah
Mpaka akumagoma ah ah
Wakumana ndi CHIPHONA ah
SUNDIKOPA kopa ase
Devil yo kumubona mmhu
Mpaka akumagoma mmhuu
Wakumana ndi CHIPHONA
SUNDIKOPA kopa ase
Ey yeay yah

Credits
Writer(s): Joy Gondwe
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Link
© 2024 All rights reserved. Rockol.com S.r.l. Website image policy
Rockol
- Rockol only uses images and photos made available for promotional purposes (“for press use”) by record companies, artist managements and p.r. agencies.
- Said images are used to exert a right to report and a finality of the criticism, in a degraded mode compliant to copyright laws, and exclusively inclosed in our own informative content.
- Only non-exclusive images addressed to newspaper use and, in general, copyright-free are accepted.
- Live photos are published when licensed by photographers whose copyright is quoted.
- Rockol is available to pay the right holder a fair fee should a published image’s author be unknown at the time of publishing.
Feedback
Please immediately report the presence of images possibly not compliant with the above cases so as to quickly verify an improper use: where confirmed, we would immediately proceed to their removal.