Moto

Ine m'mati nkolole chaka chino
Taonani mwandisiyaso ndi njala
Zindalama mukubinyila mwandisiyaso pano
Koma munkabwera muzandionesa mano
Maluzi andigwila
Koma Chauta amaona
Kodi tikati konzu muziononga
Tikati tikonze muziononga
Mukusephetsa stuff izi
Magobo timagwirawa ndiwovuta
Ine ndikonze inu mukonze
Mesa tonsefe tithandizane
Ndikumva kuwawa
Fukwa mwandilanga, zomwe mwandipanga sindizaiwala
Get a little change when you move in a moment
Now I'm looking sad cause I'm losing a moment
Never try to think that it's professional
Zomwe mwandipanga zandidetsa nkhawa
Taonani ndungokhalila kukhumudwa
Cause I'm being robed
Ndimakapewa
Zodalila ndizambili nowadays I'm too strong
Kotsamila ndi kwa iye yemwe anampatsa moyo
Kumwamba kukatseguka muzaonano moto
Katangale azatha muzakhalano kumoto
Moto
Moto
Moto (moto)
Moto
Moto
Moto (muzaonano moto)
Moto
Moto
Moto (moto)
Moto
Moto moto (muzaonano)
Moto
Moto
Mukusephetsa stuff izi
Magobo timagwirawa ndiwovuta
Ine ndikonze inu mukonze
Mesa tonsefe tithandizane
Ndikumva kuwawa
Fukwa mwandilanga, zomwe mwandipanga sindizaiwala
Get a little change when you move in a moment
Now I'm looking sad cause I'm losing a moment
Mumandipeza kwathu kuti ndizigwila ntchito
Mumabwera Mukuseka mulibenso ntchito
Eya timalima lelo takolola
Ndipatseni ndalama mukutenga zonse bwa
Ah ndalama zanga
Ndukumufuna kayesala wanga
Naneso ndimafuna ndalamazi
Ambuye azikuonani
Moto
Moto
Moto (zandidetsa nkhawa)
Moto
Moto (ndikukukhumudwa)
Moto
Moto oh Moto ohoooh
Moto oh Moto ohoooh
Moto
Moto
Moto
Moto
Moto
Moto
Moto
Moto
Moto
Moto
Moto



Credits
Writer(s): Daniel Kauma, Julio Rebelo
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link