International spe - Freestyle

Nnangodzuka mornaz ndi zi confi za ine
Nnamu talker jah jah ndizijama ya ine
Anangoti udekhe ndikupanga za iwe
11:11 i got blessings on the way
Goat wanu ati aku payer ma page
Kuti apange damage za dancehall ya ine
Ndinali ku naisi ndi ma boys ya ine
Nditaona nnangoseka ndikuzitaya ine
Rolex ili pa bwanji ino ndi nthawi ya ine
Born ready ondichedwesa ndimuthawa ine
Good vibes usandipatse nkhawa ine
International Spe iwe si makawa ine
MTV Base ku player step by step
Back to back
Sindimvela nyimbo zanu, chifukwa cha?
Ndi za whack
Cash ima talker yokha choka phwanga ulibe cash
Busy pocket watching koma dollar sili mu thumba
Ndikupanga zanga basi inu mungosilira
Mulimbe mtima guys mungopilira
Ndilipo mpaka nzachita kusankha omusiyila
Dollar ya show ingokwela ngati katapila
Best MC in mdubz
Kuyambitsa chipwilikiti pa entrance
8o8 wa beat kusokoneza neighbour
Trap bidness ku trap osabwela ndi chikheba
I'm too good at this
Iwe ukumvela ziti?
Utalker ziti?
Zaza pa repeat uku uku burner ah
Cannabis
Your GOAT can't trap like this
Zosafila spe ndizachimidzi



Credits
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link