YAYA

Ndapeza mayankho si amu nseli no
Chikondi chako sicha nseli no
Ntima wako sungapatse wina
Umandikonda my angelina
My angelina

Olo andikambile nkhani umandikondabe yaya (umandikondabe)
Olo andi sayize bwanji umandikondabe yaya (umandikondabe)

Zambili amanena kuyipitsa mbili yanga (umandikondabe)
Kundikhomelera afuna atandilanda (umandikondabe)
Koma no, iwe umandiko (umandikondabe)
Koma no, iwe umandiko (umandikondabe)

Olo angakunene bwanji
You always there you never run from me
Even though they are talking, they are stocking
They can't make you leave

Mmmh, ndakugomera
Mmmh, ndakugomera
Mmmh, ndakugomera
Mmmh, ndakugomera

Olo andikambile nkhani umandikondabe yaya (umandikondabe)
Olo andi sayize bwanji umandikondabe yaya (umandikondabe)
Olo andikambile nkhani umandikondabe yaya (umandikondabe)
Olo andi sayize bwanji umandikondabe yaya (umandikondabe)

Zambili amanena kuyipitsa mbili yanga (umandikondabe)
Kundikhomelera afuna atandilanda (umandikondabe)
Koma no, iwe umandiko (umandikondabe)
Koma no, iwe umandiko (umandikondabe)

Mmmh, ndakugomera (umandikondabe)
Mmmh, ndakugomera (umandikondabe)

Credits
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link