Superstar

(Akuzike Speaks)
I'm going to be a singer
Aaaah a superstar
And a doctor and a dentist
Tonsefe ndiongodutsa
Kumanda kumandikumbutsa
Tsiku lina aliyense adzaweva goodbye
Ndi chilungamo and we cannot deny
Siudzapuma ayi
Celebrate my life don't cry
(Don't cry)
I'm not afraid to die
But I don't wanna die young
(I don't wanna die young)
Ndili ndimaloto ambiri koma sindikugona
Ndimalimbikila nokha mutha kuona
Ndimakhala ndi mantha
Sizipezeka kuti nthawi yanga yatha
I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Cause I wanna be a superstar
(Superstar superstar)
Keep on chasing your dreams
All the times
Kumalimbikila kumaikapo mtima ndipo udzakhala superstar
(Superstar superstar)
Yes yes yoo
Tiya was gone at 26 what a life full of dreams
Ndizilimbikila what if I die young before living my dreams?
Ndingini yowawa kuona makolo akukakwilira ana
Zisakuopye panga zazikulu uli mwana
Ukupanga geli limbika utenge degree
For the record you can be the first in your family tree
Mesa ndiwe vendor limbika ndithu zizayenda
Osagiva Iwe ndi star
Osagulitsa soul not for sale property of government
Mulungu patsogolo ndipo udzakhala relevant
Idzalora Malawi
Chilichonse ndi nthawi
I don't wanna die young kapena tu kudzafa mphawi
Ndili ndimaloto ambiri koma sindikugona
Ndimalimbikila nokha mutha kuona
Ndimakhala ndi mantha
Sizipezeka kuti nthawi yanga yatha
I wanna to be a superstar
(Superstar superstar)
Cause I wanna to be a superstar
(Superstar superstar)
Keep on chasing your dreams
All the times
Kumalimbikila kumaikapo mtima ndipo udzakhala superstar
(Superstar superstar)
I wanna to be a superstar
(Superstar superstar)
Cause I wanna to be a superstar
(Superstar superstar)



Credits
Writer(s): Daniel Tadala Kasinjeni
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link