MADA (Remix) [feat. Ace Jizzy, Bee Jay, K Banton, Waxy Kay, Guntolah, Che Kalonda, Mellz Kumpanje, Jeg & Jolasto]

Yeah
It's Only Entertainment
Cuff-B Production
Sameface on the Beats
Mumakwana a Mada
Mwabhebha mwabhebha
Mwaipatsa moto a Mada
Mwatentha mwatentha

Woozzah
Akakhosomola ndekuti afuna pizza
Amadaliso nthumba mwawo sachedwa ku pisa
Issa mpaka namupangisila Viza
Nkazi oti nangokumana naye pa Instagram
Pano ndi mlamu
Mmhu am so dam
Ine nkangofuna kudya Buble gum hmmm
Murder Murder Murder Murder hmm satha kumvetaa
Pena Gena zomwe imapanga the other gender
Pakakhala Dollar imangobenda Yeah
Malo mopala moto undipalimulisa
Mabomba a rasha ndizindikila nda phulitsa
Katundu wanuyo ndikuziwa mumagulisa
Mdulidwe wazimayi kulibe nde osadulisa
Iiih aMada

Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case

Zofuna za Mada ase
Zikangolowa ku madance eti
Kugula Gin Wawa Castel
Aphula sin akangotell
Mhuu
Uyu singagwire mwa easy
Kundipasa chance singasinze
Ngati chux ndi maplan ndili busy
Kuti ukhale mula wa Jizzy
Nkazi wachi body chonyadisa
Nde sinzakubisa anthu akudziwe
Pa Facebook, Insta ndi Twitter
Ndikasintha picture pakakhala iwe
Koma MADA doesn't care
Ena ATI ndika wash and wear
Ndimamufuna kuposa mpweya
Mundilangiza ine Osamvera aaah

Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case

Ukumachita kundigwedezera matako mada
Ine si charisma pa Tuno
Aaah FADA (alipo samafuna kudya)
(mada) ine ndiofewa mchiuno
Atandimanga sangamve zokuti
Umachita kundipeza wekha kwathu kuno
Nde panopa sukumavalamo mwado (mada)
Ukumangongoyenda buno buno
Ndikati easy umati NO
Umaipatsa moto (ipondeni fadah)
Umaiwala zoti amanjata (Gwii)
Ufuna ndikalowe ndi Mada
Why you gotta do me like this mada
Ukufuna kuti ndipange commit mada
Ukupanga chani madalitso
Ufuna khoba izawatenge fada

Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case

Mpaka ndiphula ma sin kamba ka iwe Mada
Wina ndimuNYIKA ndimadana ndizaFANTA
Ndakumvela kuwawa kuti ufike apapa
Ndipo muwuzane wina ndimuchotsa mphafa
Unaponya status ukumenya nip
Sikuti ndikuku kumba ndangowona ma pic
Kuyiwala kwanu unapanga mistake
Ati Blantyre sinodi? Zawu wayilesi
Madaaa kaya unafa kwambiri
Nane ndi mfumu ndikudyesa ma tick
Ukuwonjeza my queen
Nane town ndiyanga ngati maskin
Eti uli blues? Ukumwa manica?
Ukuspendar dollar uli ndi ma nigga?
Eti zafika poti boys ikukugwila?
Ati uli ready akufunayo aika?

Mada mbuyo monsemu sinakhale case
Mwina ndili mwana kusewelesa zikhesi
Koma anthu akwathu akati napangidwa curse
Akazi ndinkagwila ngat Shammah no reverse
Nkaz opanda mbuyo
Kumandibwenza mmbuyo
Sinaphake naye life ati
Anali smoke sinatchaye olo life
Ati Samva Maloza
Chifukwa chan anaonapo maloza
Ati x wake sankapanga cholozeka
Asing'anga agwila ntchito ine ndekha ndolozeka
Koma inalipo nthawi yosowa chochitika
Ma Beat mangonyika
Asilamu akudanda ati sindipanganika
Kubwera mada kuwelama
Kuzasikana kenako kukwerana
Ndichi red sign nkona tikufilana. MADA

Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Mwana kazi undipweteka
Unditakasa Undipepeta
Ndikagona Ndiku Mbrupahur hvd
Ndiku bwebweta!
Upange zomwe wanena
Ndipo ndizione zikuthekeka
Ngati wati cheke Cheke apa!
Ndikuone ukuchekeka iiiyh
MADAm mada ukalola Ine wadya!!
MADA undimadalits
Iii taonani undibalalitsa!
Azimayi Nthungululu pamenepa!
Amanena kuti love Is blind Ine kuno khungu
Nde yandipweteka
Sindikuona komaso sindikubona undivetse

Dzina ndani? Madalitso
Ndiwe okongola ngati ku paradizo
Tabwera kuno mdzataniso?
Tiime pachulu ngati bwana Mbizzo
Ana okuposa palibetu
Or nkhalamba paliJETU
Gaire ndalama pa Easy'tu
Dollar yaine sungamalizetu
Ine ndi mponda matik
Ndimamenya mponda ma kick
Nkonda ma gig nkonda ma chick
Mada usanditole tola ma pic
Umulore MADA gangster
Honey moon ndiku MADA gascar
Ndamva zoti wakana chi namtindi
Iwe ndiine love Mwantinti

Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case

Mfana ophulitsa life ngati Makombola
Kuthamanga kwambiri kuposa Corolla
Kumuuza Kuti tiye amangolola
Chilichonse atha kupanga nabola Dolla
Nde Ali Ndi chi figure Ngati Masamu
Dzimatatoo Mbwee Mmatakomu
Wapengetsa Ma Bwana Ntaunimu
Koma Chonde Usadye Ndi Halamu
Nde Mwati iyeyu ndi Ndani (KAYA)
Wabwera Ndi Ndani, Akumwa Chani (KAYA)
Mwina Kapena Ndimupatse Plan
Mmmmh Dadda Uyu Akuchedwetsani

Akazi akalowa mu boy zone
Olimbana nao amwa poison
Bambo anga paza kuden zima weapon
Wina azakushoshe azalira Ring tone
Iwe Uzangomva ngiri ngiri
Wina azanditenge kuchigwiri gwiri
Amuna anga alusiratu kuno dada
Amuna anga atha kupalamula mada

Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case



Credits
Writer(s): Noel Phyzix Chikoleka
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link