KUMVANA

Koma ndimene zinthu zililimu, ngini ililimu
Paliponse anthu akunvana
Kunvana kunvana anywhere
Kweni kweni zoti anthu azatheka mukunama

Timafuna malo asukulu a head
Titha kunvana
Mayala mwavalawo mwatchena breda
Titha kunvana
Iwe bwanji diso lako lili red
Titha kunvana mayalawavalawo mwatchena Breda
Titha kunvana

Ndikuziwa uli pabanja (i know)
Koma titha kunvana
Ndanva zoti amuna ako akupanga matama
24/7 ati mumakangana
Nde titha kungopanga zoti tizingomvana
Kumvana kumvana ngati amalawi ndi Maury
Kunvana kunvana ngati wanchenga ndi lorry
Koma ngati palibe dolla sindinga role
Malo opanda moto ine sindingapore
Okay its all about connections men am not gonna Lie
Kumvana ndimalasi kuti nzikhala high kumvana Ndimuluya kuti ndifike dubai
Kunvana ndi HR nkamapanga apply

Koma ndimene zinthu zililimu, ngini ililimu
Paliponse anthu akunvana
Kunvana kunvana anywhere
Kweni kweni zoti anthu azatheka mukunama

Timafuna malo asukulu a head
Titha kunvana
Mayala mwavalawo mwatchena breda
Titha kunvana
Iwe bwanji diso lako lili red
Titha kunvana mayalawavalawo mwatchena Breda
Titha kunvana

Hustle yosamvana nde ndi hustle yabwanji
Hgini ndaikonda osangochosera bwanji
Ukufuna 10 pin nanga last ndibwanji
Pali ka 4pin tionjezelepo bwanji
Kumvana kumvana zikungothera kumvana
Tikapanda kumvana zingothera mambama
Ikapanga zomvana ghetto imakungana
Ndimapephela tisananvane kuti ndichose Minyama
Its all about connections men am not gonna lie
Kumvana ndimalasi kuti nzikhala high
Kumvana ndimuluya kuti ndifike Dubai
Kumvana ndi HR nkamapanga apply

Koma ndimene zinthu zililimu, ngini ililimu
Paliponse anthu akunvana
Kunvana kunvana anywhere
Kweni kweni zoti anthu azatheka mukunama

Timafuna malo asukulu a head
Titha kunvana
Mayala mwavalawo mwatchena breda
Titha kunvana
Iwe bwanji diso lako lili red
Titha kunvana mayalawavalawo mwatchena Breda
Titha kunvana



Credits
Writer(s): Emm Zibry
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link