Nyimbo Ya Chikondi (feat. Ace Jizzy)

Ase (yeah)
Babe yathu ikuti
Timangoyimba
Za mavuto chani chani
Nde tiyimbe ka nyimbo ka love song wayiziwa eti
Koma osati ija yokuti Ndakudalila
Mhuu Wayiziwa imene ija
Ingokhala inayake ija wayiziwa
Ndizimenya ma Yahman yah
(Kumabwera ma) nkhani yake Yabanja
Chani chani chani chani chani Yapanja
Eheee

Bae (yahman yah)
Ndibwera kwanu azandiziwe (amama)
Wakonda JEG kusiya guy (ya ndlama)
Ili ndi bima,jeep (ndi hammer)
Ine dentist ndine Mfana (wa Khama)
Ndiwe wabho sundipangilA (matama)
Siwe Traore monga ma bebi (ADama)
Ngawu Monada amakonda zo (gadama)

Pa den ndizakuphikra (phwanyanya)
Mipunga mipiru (khwanyanya)
Pa nkhani yokongolayi (unanyanya)
Pokwana unadusa uma (kwanyanya)
Enawa zimawa di (nyanyanya)
Zoti umawa chi (nyanyanya)
Koma ndizawa fi (nyanyanya)
Ndimadana ndizopusa za (nyonyonyo)

Umafilla nyimbo za Chikondi
Nkhani ndabwera nayo rose
Zokutuluka nde ndi Ngozi
Tanena mhhu Eh
Wati umafilla nyimbo za Chikondi - (Yahman yah)
Nkhani ndabwera nayo rose - (njabanja)
Zokutuluka nde ndi Ngozi - (nzapanja)
Tanena mhhu Eh

Akazi enawa akuchepela kababa
Ndaganiza zokutengela kwa baba
Chifukwa mitima yathu wababa
Ifeyo akuchimuna tikudabwa bwa
Sine player Idana olo Gaba
Sine wa ndale Nankhumwa olo Ntaba
Nkhawa zanga wafufuta rubber ber
Iyi ndi love ya Ghetto Kabwababwa

Eko Chikondi iwe cha Phamwamwa
Chikukwana tsiku lonse mpaka utsamwa
Suli ngati akazi otokota Akamwa
Umadana ndi za nkutu zamkamwa
Ndipatse kiss mhuu Mwa mwa mwa
Bwerani boiz muzawaziwe alamu anu
Honey moon izayambila Balaka, kuvaya ku Lusaka
Kukathela Panama

Umafilla nyimbo za Chikondi
Nkhani ndabwera nayo rose
Zokutuluka nde ndi Ngozi
Tanena mhhu Eh
Wati umafilla nyimbo za Chikondi - (Yahman yah)
Nkhani ndabwera nayo rose - (njabanja)
Zokutuluka nde ndi Ngozi - (nzapanja)
Tanena mhhu Eh
Umafilla nyimbo za Chikondi
Nkhani ndabwera nayo rose
Zokutuluka nde ndi Ngozi
Tanena mhhu Eh
Wati umafilla nyimbo za Chikondi - (Yahman yah)
Nkhani ndabwera nayo rose - (njabanja)
Zokutuluka nde ndi Ngozi - (nzapanja)
Tanena mhhu Eh

Aaah mhhu
Nde ma guy
Nkazi wanga video call nde ayi ayi
Muzimupasa moni yekha ndi babayi
Mukationa muzikwapuka walayi
Walayi?
Sinkhazayi
Koma namuvutikilatu mwanayi
Ankachita kumati lero ndikanayi
Wandikwezapo njinga katatu mtsikanayi
Ase Jizzy, si Kanayi?
Mhhu kaya



Credits
Writer(s): Joy Gondwe, George Nyasulu
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link