Taonani Chikondi

Taonani chikondicho
Atate wapatsa
Kwa ife anthu ochimwa
Titchedwe anake

Taonani chikondi
Chikondi icho Atate watipatsa ife
Kuti titchedwe ife
Ana ake a Mlungu

Ndipo yense wakukhala
Nacho che'mbekezo
Adzikanize yekhayo
Monga anatero

Taonani chikondicho
Atate wapatsa
Kuti ife titchedwe a-
-na a Mlungu
Ana ake a Mlungu



Credits
Writer(s): M. ş. ş.
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link