Kufuna Mtendere

Kufuna mtendere ndi chikhulupiro
Wakhala uli kupemphera
Koma nzosatheka kupeza mtendere
Mpaka utasiya tchimolo

Wapereka tchimo lako paguwalo?
Mzimu ali mtima mwako?
Ungadalitsidwe ndi mtendere wake
Ukampatsa Yesu mtimawo

Uyende ndi Mbuye mkuwala kwakeko
Kuti ukhale mu mtendere
Chita mawu ake kuti umasuke
Tula zonse pa guwa lake

Wapereka tchimo lako paguwalo?
Mzimu ali mtima mwako?
Ungadalitsidwe ndi mtendere wake
Ukampatsa Yesu mtimawo

Wapereka tchimo lako paguwalo?
Mzimu ali mtima mwako?
Ungadalitsidwe ndi mtendere wake
Ukampatsa Yesu mtimawo
Ukampatsa Yesu
Mtimawo



Credits
Writer(s): Hymnal
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link