Monga Nkhosa

Monga nkhosa tasochera
Aliyense njira yake
Tchimo maganizo (ndi) mau
Zoipa zili pa Mwana Mwana Nkhosa

Oipa asiye njira yake
Ndi ochimwa ganizo lake
Abwelere kwa Mbuye
Ndipo adzakhululukadi
Abwelere kwa Mbuye
Ndipo adzakhululukadi

Imva kupfuula kwa Mplumutsiyo
Anthu anga muferanji
Mutaya mphamvu mzoipa
Pamkate osakhutitsa

Oipa asiye njira yake
Ndi ochimwa ganizo lake
Abwelere kwa Mbuye
Ndipo adzakhululukadi
Abwelere kwa Mbuye
Ndipo adzakhululukadi



Credits
Writer(s): Esau Samu
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link