Muntima

Mumtima mwanga ndikondwa
Ndayanjananso ndi Yesu
Wandilumikizitsanso
Mumtima mwanga ndikondwa

Chimwemwe mumtima mwanga
Machimo wandichotsera
Yesu wandipulumutsa
Mumtima mwanga ndikondwa

Tchimo wakhululukira
Moyo osatha apatsa
Dzanditenga ndinke m'mwamba
Mumtima mwanga ndikondwa

Chimwemwe mumtima mwanga
Machimo wandichotsera
Yesu wandipulumutsa
Mumtima mwanga ndikondwa

Chimwemwe mumtima mwanga
Machimo wandichotsera
Yesu wandipulumutsa
Mumtima mwanga ndikondwa



Credits
Writer(s): Esau Samu
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link