Azanga

Azanga azanga azanga awa
Inuso ndi azanu awa
Azanu azanu azanuwa
Ineso ndi azanga awa
Anandilengeza mudzi Muno
Kuti ndiwalanda mamuna
Adanena inu Kwa anthu
Wa mabodza ndine basi
Akati ndikawafuna amuna awo aja
Umbeta wangawu
Wandionesa zithu
Akati ndiwabera katundu
Ndiwadanisa Kwa anthu
Sindikugwira ntchito
Mkazi wanga amandikondera chani
Mamuna opanda chochita
Angotaya nane nthawi
Agona nazo ndi njala
Mavuto samuthera
Akandiyimbira foni matu
Nkhani yake ndiwatenge ku mowa
Mpano kayimba foni
Amati ali busy
Ndine okwana ndipeze chochita
Amacheza nane tikakumana
Tikasiyana nkhani ndi yanga
Ma fake friends onsewa awa
Amandikonda ndikagula bawa awa
Andithirira coffee mu tea
Andikanika ndine chinkhonkhombe
Ana onsewa ndithyola nthiti
Akuziyesa afika pa ya ushasha
Ayiwale zoti sadumpha msewu aswiswiri



Credits
Writer(s): Innocent Chimkwapuloh
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link