Ndekha

Ndatopa kukhala ndekha
Nthawi zambiri ndekha ndekha
Anthu kumangoti chiyenda yekha
Ena kuyesa ndi kanga ndiwamba
Adona ndivereniko chisoni
Moyo sukukoma ngati kale
Ndikumasangalala ndikakhala ku ntchito
Ndikaweruka nkhawa mbwembwembwe
Enawa angowona ndalama Chilembwe
Tsiku lina ana abwerese
Ndidzawaoneko lija ndi kale
Chikondi chathu chisangalase
Chakudya sichikukoma ngati kale
Aneba akundisowesa mtendere
Tsiku ndi tsiku angojama yanga
Akundizusa mpakati pa utsiku eti
Chikondi changa chenicheni Nambewe
Ndine munthu ndimalakwitsa nthawi zina
Iwe ndi ine mpaka kale
Sindizayendaso ndi Edina
Ndavomereza njira za kale ndasiya
Kusatizira amfumu kuledzera
Wa chikondi wako ndi oyamba
Lero ndisaname ndakhulupira
Enawa angondidoda ngati mpira
Unandikonda tiri pa ulova
Enawa angowona ndalama
Amvekere i do love you dad



Credits
Writer(s): Innocent Chimkwapuloh
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link