Chiyembekezo
Chiyembekezo chodala chomwe tili nacho ife
Mwana munthu adza kudzatitenga ife kunka nafe m'mwambaa
Zakale zonse zapita zatsala za tsopano tili ndi chiyembekezo mwana munthu adza
Mwana munthu adzaa (mwana munthu adza) kudza mulemelero (kudzatitenga ife) (kudza mulemelero)
Mwana munthu adzaa (mwana munthu adza) Kudzatitenga ifeee (Kudzatitenga ife) (kudza mumitambo)
Zakale zonse zapita zatsala za tsopano tili ndi chiyembekezo
mwana munthu adza

Zizindikiro ponseponse zinena kuti mwana munthu adzaa njala nthenda usiwaa mtundu kuwukiranaaa osamusiya Yesu tiyende naye nthawi zonsee tili ndi chiyembekezo mwana munthu adzaaa
Mwana munthu adzaaa (mwana munthu adza) kudza mulemelerooo (kudzatitenga ife) (kudza mumitambo)
Mwana munthu adzaa (mwana munthu adza) Kudzatitenga ife ife ife eee(Kudzatitenga ife)

Mwana munthu adzaa (mwana munthu adza) kudzaaa mulemelerooo (kudzatitenga ife) (kudza mulemelero)

Mwana munthu adzaa

Credits
Writer(s): Thokozile Msiska
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Link
© 2025 All rights reserved. Rockol.com S.r.l. Website image policy
Rockol
- Rockol only uses images and photos made available for promotional purposes (“for press use”) by record companies, artist managements and p.r. agencies.
- Said images are used to exert a right to report and a finality of the criticism, in a degraded mode compliant to copyright laws, and exclusively inclosed in our own informative content.
- Only non-exclusive images addressed to newspaper use and, in general, copyright-free are accepted.
- Live photos are published when licensed by photographers whose copyright is quoted.
- Rockol is available to pay the right holder a fair fee should a published image’s author be unknown at the time of publishing.
Feedback
Please immediately report the presence of images possibly not compliant with the above cases so as to quickly verify an improper use: where confirmed, we would immediately proceed to their removal.