Masewera Palibe

Masewera palibe ine ndamanga lambaa udzisewera wekha ine ngwakumwamba
Uchimowo ndasiya zonse zija ndaleka nthawi yakwana tipite m'mwamba

Atikokera m'mbuyoo atikoka ngalawaa tipalasire palasire kuja kudoko

Uchimowo ndasiya ndamulandira Yesuyo nthawi yakwana tipite m'mwamba

Ah nthawi yakwana tipite m'mwamba
A-a-ah nthawi yakwana tipite m'mwamba
M'mwambaaa

Credits
Writer(s): Mphatso Chipandula
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link