Idzani

Nditamdziwa Yesuyo anandibvuula mmatope nandikhazikitsa pathanthwe nachotsa vuto langa

Idzani Idzani olema othodwa Idzani mudzapume mwa Yesu lero

Utamdziwa Yesuyo adzakubvuula mmatope nakukhazikitsa pathanthwe nachotsa vuto lako

Mudzapume mwa Yesu lero
Mudzapume mwa Yesu lero
Mudzapume mwa Yesu lero

Credits
Writer(s): Blessings Msiska
Lyrics powered by www.musixmatch.com

Link